Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 18:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Yetero anali atatumiza uthenga kwa Mose kuti, “Ine Yetero, mpongozi wako, ndikubwera ndi mkazi wako ndi ana ake awiri.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 nati kwa Mose, Ine mpongozi wako Yetero ndadza kwa iwe, ndi mkazi wako, ndi ana ake omwe awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 nati kwa Mose, Ine mpongozi wako Yetero ndadza kwa iwe, ndi mkazi wako, ndi ana ake omwe awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Munthu wina adakauza Mose kuti, “Mpongozi wanu Yetero akubwera ndi mkazi wanu ndi ana anu aŵiri aamuna.”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 18:6
3 Mawu Ofanana  

Yetero, mpongozi wa Mose pamodzi ndi ana a Mose aamuna awiri ndi mkazi wake anabwera kwa Mose ku chipululu pa phiri la Mulungu kumene Mose anamanga misasa.


Kotero Mose anatuluka kukakumana ndi mpongozi wake ndipo anawerama ndi kupsompsona. Atalonjerana anakalowa mu tenti


Kotero Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake aamuna, ndipo anawakweza pa bulu nayamba ulendo wobwerera ku Igupto. Ndipo anatenga ndodo ya Mulungu ija mʼdzanja lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa