Eksodo 18:3 - Buku Lopatulika3 dzina la winayo ndiye Geresomo, pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 dzina la winayo ndiye Geresomo, pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yetero adabweranso ndi ana aamuna aŵiri aja a Zipora. Mwana woyamba Mose adaamutcha Geresomo (chifukwa adati, “Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo.”) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 mwana wake wamkaziyo pamodzi ndi ana ake aamuna awiri. Mose anamupatsa mwana wachisamba dzina loti Geresomu popeza anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.” Onani mutuwo |