Eksodo 18:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ake awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ake awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Motero adabwera ndi Zipora, mkazi wa Mose, amene Moseyo anali atamsiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mose atamubweza Zipora, mkazi wake, Yetero, mpongozi wake anamulandira Onani mutuwo |