Eksodo 18:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mose atamubweza Zipora, mkazi wake, Yetero, mpongozi wake anamulandira Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ake awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ake awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Motero adabwera ndi Zipora, mkazi wa Mose, amene Moseyo anali atamsiya. Onani mutuwo |