Eksodo 18:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 mwana wake wamkaziyo pamodzi ndi ana ake aamuna awiri. Mose anamupatsa mwana wachisamba dzina loti Geresomu popeza anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.” Onani mutuwoBuku Lopatulika3 dzina la winayo ndiye Geresomo, pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 dzina la winayo ndiye Geresomo, pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yetero adabweranso ndi ana aamuna aŵiri aja a Zipora. Mwana woyamba Mose adaamutcha Geresomo (chifukwa adati, “Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo.”) Onani mutuwo |