Eksodo 14:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Farao adzanena za ana a Israele, Azimidwa dziko, chipululu chawatsekera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Farao adzanena za ana a Israele, Azimidwa dziko, chipululu chawatsekera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Apo Farao adzaganiza kuti, ‘Aisraele asokonezeka, akungoyendayenda m'dzikomo, azingidwa ndi chipululu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Farao adzaganiza kuti ‘Aisraeli asokonezeka nʼkumangozungulirazungulira mu dzikomo, chipululu chitawazinga.’ Onani mutuwo |