Eksodo 10:16 - Buku Lopatulika16 Pamenepo Farao anafulumira kuitana Mose ndi Aroni; nati, Ndalakwira Yehova Mulungu wanu, ndi inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pamenepo Farao anafulumira kuitana Mose ndi Aroni; nati, Ndalakwira Yehova Mulungu wanu, ndi inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndipo Farao adaitana Mose ndi Aroni mofulumira naŵauza kuti, “Ndachimwira Chauta, Mulungu wanu, ndipo ndachimwiranso inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mwamsangamsanga, Farao anayitanitsa Mose ndi Aaroni ndipo anati, “Ine ndachimwira Yehova Mulungu wanu ndiponso inu. Onani mutuwo |