Eksodo 10:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo tsopano, ndikhululukiretu kulakwa kwanga nthawi ino yokha, nimundipembere kwa Yehova Mulungu wanu, kuti andichotsere imfa ino yokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo tsopano, ndikhululukiretu kulakwa kwanga nthawi yino yokha, nimundipembere kwa Yehova Mulungu wanu, kuti andichotsere imfa yino yokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma pepani tsopano, khululukireni pa nthaŵi ino yokha, mupemphe kwa Chauta, Mulungu wanu, kuti andichotsere chilango choopsachi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Tsopano ndikhululukirenso tchimo langa kano konkha ndipo pempherani kwa Yehova Mulungu wanu kuti andichotsere mliri wosakazawu.” Onani mutuwo |