Danieli 4:5 - Buku Lopatulika5 Ndinaona loto lakundiopsa, ndi zolingirira za pakama panga, ndi masomphenya a m'mtima mwanga, zinandivuta ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndinaona loto lakundiopsa, ndi zolingirira za pakama panga, ndi masomphenya a m'mtima mwanga, zinandivuta ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndili chigonere pa bedi langa, ndinalota maloto amene anandichititsa mantha. Zinthu ndi masomphenya zimene ndinaziona zinandiopsa. Onani mutuwo |