Danieli 4:4 - Buku Lopatulika4 Ine Nebukadinezara ndinalimkupumula m'nyumba mwanga, ndi kukhala mwaufulu m'chinyumba changa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ine Nebukadinezara ndinalimkupumula m'nyumba mwanga, ndi kukhala mwaufulu m'chinyumba changa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ine Nebukadinezara, ndinali kwathu mʼnyumba yanga yaufumu, mwa mtendere ndipo ndinali wokhutitsidwa. Onani mutuwo |