Danieli 4:6 - Buku Lopatulika6 Chifukwa chake ndinalamulira kuti adze kwa ine anzeru onse a ku Babiloni, kuti andidziwitse kumasulira kwake kwa lotoli. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chifukwa chake ndinalamulira kuti adze kwa ine anzeru onse a ku Babiloni, kuti andidziwitse kumasulira kwake kwa lotoli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho ndinalamula kuti anthu onse a nzeru a ku Babuloni abwere pa maso panga kunditanthauzira malotowo. Onani mutuwo |