Danieli 2:13 - Buku Lopatulika13 M'mwemo chilamulirocho chidamveka, ndi eni nzeru adati aphedwe; anafunafunanso Daniele ndi anzake aphedwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 M'mwemo chilamulirocho chidamveka, ndi eni nzeru adati aphedwe; anafunafunanso Daniele ndi anzake aphedwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Choncho lamulo linaperekedwa kuti anthu anzeru aphedwe, ndipo anatuma anthu kukafunafuna Danieli ndi anzake kuti iwonso aphedwe. Onani mutuwo |