Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Afilipi 4:16 - Buku Lopatulika

16 pakuti mu Tesalonikanso munanditumizira pa chosowa changa kamodzi kapena kawiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 pakuti m'Tesalonikanso munanditumizira pa chosowa changa kamodzi kapena kawiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Pamene ndinali ku Tesalonika, mudatumiza kangapo zondithandiza pa zosoŵa zanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Pakuti ngakhale pamene ndinali ku Tesalonika, munanditumizira kangapo zondithandiza pa zosowa zanga.

Onani mutuwo Koperani




Afilipi 4:16
4 Mawu Ofanana  

Pamene anapitirira pa Amfipoli, ndi Apoloniya, anafika ku Tesalonika, kumene kunali sunagoge wa Ayuda.


chifukwa tinafuna kudza kwa inu, inedi Paulo ndatero kamodzi kapena kawiri; koma Satana anatiletsa.


Pakuti mukumbukira, abale, chigwiritso chathu ndi chivuto chathu; pochita usiku ndi usana, kuti tingalemetse wina wa inu, tinalalikira kwa inu Uthenga Wabwino wa Mulungu.


Ndipo anthu athu aphunzirenso asunge ntchito zabwino zofunika, kuti asakhale osabala zipatso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa