Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 4:3 - Buku Lopatulika

3 ndi Abeeroti anathawira ku Gitaimu; kumeneko amakhalira kufikira lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 ndi Abeeroti anathawira ku Gitaimu; kumeneko amakhalira kufikira lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Abeeroti adathaŵira ku Gitaimu, ndipo akhala akukhala nao kumeneko mpaka pano).

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 chifukwa anthu a ku Beeroti anathawira ku Gitaimu ndipo akhala ali kumeneko ngati alendo mpaka lero lino.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 4:3
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Yonatani mwana wa Saulo, anali ndi mwana wamwamuna wopunduka mapazi. Iyeyu anali wa zaka zisanu muja inamveka mbiri ya Saulo ndi Yonatani yochokera ku Yezireele; ndipo mlezi wake adamnyamula nathawa; ndipo kunali pofulumira kuthawa, iye anagwa nakhala wopunduka. Dzina lake ndiye Mefiboseti.


Hazori, Rama, Gitaimu,


Ndipo pamene Aisraele akukhala tsidya lina la chigwa, ndi iwo akukhala tsidya la Yordani, anaona kuti Aisraele alikuthawa, ndi kuti Saulo ndi ana ake anafa, iwowa anasiya mizinda yao, nathawa; ndipo Afilisti anadza nakhala m'menemo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa