2 Samueli 24:8 - Buku Lopatulika8 Chomwecho pamene atayenda dziko lonse anafika ku Yerusalemu pakutha miyezi isanu ndi inai, ndi masiku makumi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chomwecho pamene atayenda dziko lonse anafika ku Yerusalemu pakutha miyezi isanu ndi inai, ndi masiku makumi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Motero, atabzola dziko lonselo, adadzafika ku Yerusalemu itatha miyezi isanu ndi inai ndi masiku makumi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Atayendayenda mʼdziko lonse anabwerera ku Yerusalemu patapita miyezi isanu ndi inayi ndi masiku makumi awiri. Onani mutuwo |