Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 24:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Atayendayenda mʼdziko lonse anabwerera ku Yerusalemu patapita miyezi isanu ndi inayi ndi masiku makumi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Chomwecho pamene atayenda dziko lonse anafika ku Yerusalemu pakutha miyezi isanu ndi inai, ndi masiku makumi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Chomwecho pamene atayenda dziko lonse anafika ku Yerusalemu pakutha miyezi isanu ndi inai, ndi masiku makumi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Motero, atabzola dziko lonselo, adadzafika ku Yerusalemu itatha miyezi isanu ndi inai ndi masiku makumi aŵiri.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 24:8
2 Mawu Ofanana  

Kenaka iwo anapita molunjika linga la ku Turo ndi ku mizinda yonse ya Ahivi ndi Akanaani. Pomaliza anapita ku Beeriseba ku Negevi wa ku Yuda.


Yowabu anapereka chiwerengero cha anthu ankhondo kwa mfumu: Mu Israeli munali anthu 800,000 amphamvu amene amadziwa kugwiritsa ntchito lupanga ndipo mu Yuda munali anthu 500,000.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa