2 Samueli 24:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yowabu anapereka kwa mfumu kuchuluka kwa anthu adawawerenga; ndipo mu Israele munali anthu zikwi mazana asanu ndi atatu, ngwazi zosolola lupanga; ndi anthu a Yuda ndiwo zikwi mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yowabu anapereka kwa mfumu kuchuluka kwa anthu adawawerenga; ndipo m'Israele munali anthu zikwi mazana asanu ndi atatu, ngwazi zosolola lupanga; ndi anthu a Yuda ndiwo zikwi mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono Yowabu adapereka chiŵerengero cha anthu onse kwa mfumu. Ku dziko la Israele kunali anthu 800,000 otha kumenya nkhondo, ndipo ku Yuda kunali 500,000 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yowabu anapereka chiwerengero cha anthu ankhondo kwa mfumu: Mu Israeli munali anthu 800,000 amphamvu amene amadziwa kugwiritsa ntchito lupanga ndipo mu Yuda munali anthu 500,000. Onani mutuwo |