2 Samueli 22:6 - Buku Lopatulika6 Zingwe za kumanda zinandizingira; misampha ya imfa inandifikira ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Zingwe za kumanda zinandizingira; misampha ya imfa inandifikira ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nthambo zakumanda zidandizeŵeza, misampha ya imfa idandikola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Anandimanga ndi zingwe za ku manda; misampha ya imfa inalimbana nane. Onani mutuwo |