Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 22:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Anandimanga ndi zingwe za ku manda; misampha ya imfa inalimbana nane.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Zingwe za kumanda zinandizingira; misampha ya imfa inandifikira ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Zingwe za kumanda zinandizingira; misampha ya imfa inandifikira ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Nthambo zakumanda zidandizeŵeza, misampha ya imfa idandikola.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 22:6
10 Mawu Ofanana  

Koma ngati anthu amangidwa ndi unyolo, ndipo akondwa ndi zingwe zamasautso,


Zingwe za imfa zinandizinga, zoopsa za ku dziko la anthu akufa zinandigwera; ndinapeza mavuto ndi chisoni.


Anthu odzikuza anditchera msampha mobisika; iwo atchera zingwe za maukonde awo ndipo anditchera misampha pa njira yanga. Sela


Anandimanga ndi zingwe za ku manda; misampha ya imfa inalimbana nane.


Malangizo a munthu wanzeru ali ngati kasupe wamoyo; amathandiza munthu kuti asakondwe mu msampha wa imfa.


Kuopa Yehova ndiye kasupe wamoyo, kumathandiza munthu kuti apewe msampha wa imfa.


Ntchito zoyipa za munthu woyipa zimamukola yekha; zingwe za tchimo lake zimamumanga yekha.


Iye anati: “Pamene ndinali mʼmavuto anga ndinayitana Yehova, ndipo Iye anandiyankha. Ndili ku dziko la anthu akufa ndinapempha thandizo, ndipo Inu munamva kulira kwanga.


“Mukadzaona Yerusalemu atazingidwa ndi magulu ankhondo, inu mudzadziwe kuti kuwonongeka kwake kuli pafupi.


Koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, kumumasula Iye ku zowawa za imfa, chifukwa kunali kosatheka kuti agwiridwe ndi imfa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa