Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 22:50 - Buku Lopatulika

50 Chifukwa chake ndidzakuongani Yehova, pakati pa amitundu, ndipo ndidzaimba zolemekeza dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

50 Chifukwa chake ndidzakuongani Yehova, pakati pa amitundu, ndipo ndidzaimba zolemekeza dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

50 “Chifukwa cha zimenezi ndidzakuyamikani Inu Chauta, pakati pa mitundu ya anthu, ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

50 Choncho ine ndidzakutamandani Inu Yehova, pakati pa anthu a mitundu ina; ndidzayimba nyimbo zotamanda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 22:50
7 Mawu Ofanana  

Iye apatsa mfumu yake chipulumutso chachikulu; naonetsera chifundo wodzozedwa wake, kwa Davide ndi mbeu yake ku nthawi zonse.


Pakuti chifundo chanu nchachikulu kupitirira kumwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.


Chifukwa chake Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu, ndipo dzina lanu ndidzaliimbira.


ndi kuti anthu a mitundu ina akalemekeze Mulungu, chifukwa cha chifundo; monga kwalembedwa, Chifukwa cha ichi ndidzakuvomerezani Inu pakati pa anthu amitundu, ndidzaimbira dzina lanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa