2 Samueli 22:48 - Buku Lopatulika48 inde Mulungu wakundibwezera chilango ine, ndi kundigonjetsera anthu a mitundu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 inde Mulungu wakundibwezera chilango ine, ndi kundigonjetsera anthu a mitundu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Mulungu ndiye adandithandiza kuti ndilipsire, ndi kugonjetsa anthu a mitundu ina kuti akhale mu ulamuliro wanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Iye ndi Mulungu amene amabwezera chilango, amene amayika anthu a mitundu yonse pansi pa ulamuliro wanga, Onani mutuwo |
Ndipo pamene Davide anamva kuti Nabala adamwalira, iye anati, Alemekezedwe Yehova, amene anaweruza mlandu wa mtonzo wanga wochokera ku dzanja la Nabala, naletsa mnyamata wake pa choipa; ndipo Yehova anabwezera pamutu pa Nabala choipa chake. Ndipo Davide anatumiza wokamfunsira Abigaile, zakuti amtengere akhale mkazi wake.