2 Samueli 22:47 - Buku Lopatulika47 Yehova ali ndi moyo; ndipo lidalitsike thanthwe langa; ndipo akulitsidwe Mulungu wa thanthwe la chipulumutso changa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Yehova ali ndi moyo; ndipo lidalitsike thanthwe langa; ndipo akulitsidwe Mulungu wa thanthwe la chipulumutso changa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 “Chauta ndiwamoyo. Litamandike thanthwe langa, alemekezeke Mulungu wanga, thanthwe londipulumutsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 “Yehova ndi wamoyo! Litamandidwe Thanthwe langa. Akuzike Mulungu, Thanthwe, Mpulumutsi wanga! Onani mutuwo |