2 Samueli 22:46 - Buku Lopatulika46 Alendo adzafota, nadzabwera ndi kunthunthumira otuluka mokwiririka mwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 Alendo adzafota, nadzabwera ndi kunthunthumira otuluka mokwiririka mwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 Anthu a mitundu ina adataya mtima, adatuluka m'malinga mwao ali njenjenje. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 Iwo onse anataya mtima; anatuluka mʼmalinga awo akunjenjemera. Onani mutuwo |