2 Samueli 22:45 - Buku Lopatulika45 Alendo adzandigonjera ine, pakumva za ine, adzandimvera pomwepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Alendo adzandigonjera ine, pakumva za ine, adzandimvera pomwepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Anthu a maiko ena adabwera kwa ine kudzapemba; atangomva mau anga oyamba adandimvera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Alendo amadzipereka okha pamaso panga; akangomva za ine, amandigonjera. Onani mutuwo |