2 Samueli 22:43 - Buku Lopatulika43 Pomwepo ndinawasansantha asalale ngati fumbi la padziko, ndinawapondereza ngati dothi la m'makwalala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Pomwepo ndinawasansantha asalale ngati fumbi la padziko, ndinawapondereza ngati dothi la m'makwalala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Ndidaŵaperapera ngati fumbi, ndidaŵaphwanya ndi kuŵapondereza ngati matope amumseu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Ine ndinawaperesa ngati fumbi la pa dziko lapansi; ndinawasinja ndipo ndinawapondaponda ngati matope a mʼmisewu. Onani mutuwo |