2 Samueli 22:42 - Buku Lopatulika42 Anayang'ana iwo, koma panalibe wopulumutsa; ngakhale kwa Yehova, koma Iye sanawayankhe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Anayang'ana iwo, koma panalibe wopulumutsa; ngakhale kwa Yehova, koma Iye sanawayankhe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Adakuwa, koma panalibe ndi mmodzi yemwe woŵapulumutsa. Adalirira Chauta, koma sadaŵayankhe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Iwo anafuwula kupempha thandizo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe owapulumutsa. Analirira kwa Yehova, koma sanawayankhe. Onani mutuwo |