2 Samueli 22:41 - Buku Lopatulika41 Munatembenuzitsanso adani anga andipatse mbuyo, kuti ndiwalikhe akudana ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Munatembenuzitsanso adani anga andipatse mbuyo, kuti ndiwalikhe akudana ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Inu mudapirikitsa adani anga kuti andithaŵe, amene ankadana nane ndidaŵaononga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Inu muchititsa kuti adani anga atembenuke ndi kuthawa; ndipo ndinawononga adani anga. Onani mutuwo |