2 Samueli 22:40 - Buku Lopatulika40 Pakuti Inu munandimanga m'chuuno ndi mphamvu ya kunkhondo; munandigonjetsera akundiukira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Pakuti Inu munandimanga m'chuuno ndi mphamvu ya kunkhondo; munandigonjetsera akundiukira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Paja ndinu mudandipatsa mphamvu zomenyera nkhondo, ndinu mudandigonjetsera anthu ondiwukira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Inu munandipatsa ine mphamvu yochitira nkhondo; munagwaditsa adani anga pa mapazi anga. Onani mutuwo |