2 Samueli 22:38 - Buku Lopatulika38 Ndinapirikitsa adani anga, ndi kuwaononga; ndiponso sindinabwerere mpaka nditawatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndinapirikitsa adani anga, ndi kuwaononga; ndiponso sindinabwerera mpaka nditawatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Ndidalondola adani anga ndi kuŵapeza, sindidabwerere mpaka nditaŵagonjetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 “Ine ndinathamangitsa adani anga ndi kuwakantha; sindinabwerere mpaka iwo atawonongedwa. Onani mutuwo |