2 Samueli 22:37 - Buku Lopatulika37 Munakulitsa kulunza kwanga pansi panga, ndi mapazi anga sanaterereke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Munakulitsa kulunza kwanga pansi panga, ndi mapazi anga sanaterereke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Mwalimbitsa miyendo yanga kuti ndiyende bwino, choncho mapazi anga sadaterereke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Inu mwalimbitsa njira yanga kuti ndiyende bwino, kuti mapazi anga asaterereke. Onani mutuwo |