2 Samueli 22:36 - Buku Lopatulika36 Ndiponso munandipatsa chikopa cha chipulumutso chanu; ndi kufatsa kwanu kunandikulitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndiponso munandipatsa chikopa cha chipulumutso chanu; ndi kufatsa kwanu kunandikulitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Inu mwanditeteza ndi chishango chanu chachipulumutso. Mwandikweza ndi chithandizo chanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Inu mundipatsa ine chishango chanu cha chigonjetso; mumawerama kuti mundikweze. Onani mutuwo |