Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 22:35 - Buku Lopatulika

35 Iye aphunzitsa manja anga nkhondo; kotero kuti manja anga alifula uta wamkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 Iye aphunzitsa manja anga nkhondo; kotero kuti manja anga alifula uta wamkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 Amaphunzitsa manja anga kamenyedwe ka nkhondo, kotero kuti ndingathe kupinda uta wachitsulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Iye amaphunzitsa manja anga kuchita nkhondo; manja anga amatha kuthyola uta wachitsulo.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 22:35
7 Mawu Ofanana  

Adzathawa chida chachitsulo, ndi muvi wa uta wamkuwa udzampyoza.


Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, wakuphunzitsa manja anga achite nkhondo, zala zanga zigwirane nao:


Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.


ndipo ndidzakantha uta wako kuuchotsa m'dzanja lako lamanzere, ndi kutayitsa mivi yako kudzanja lako lamanja.


Ndipo Davide anati kwa Mfilistiyo, Iwe ukudza kwa ine ndi lupanga, ndi mkondo, ndi nthungo; koma ine ndafika kwa iwe m'dzina la Yehova wa makamu, Mulungu wa ankhondo a Israele amene iwe unawanyoza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa