Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 22:34 - Buku Lopatulika

34 Iye asandutsa mapazi ake akunga mapazi a mbawala; nandiika pa misanje yanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Iye asandutsa mapazi ake akunga mapazi a mbawala; nandiika pa misanje yanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Amalimbitsa mapazi anga ngati a mbaŵala, ndipo amandisunga bwino ku mapiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Iye amasandutsa mapazi anga kukhala ngati ambawala yayikazi; Iye amandithandiza kuyimirira pamwamba pa mapiri.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 22:34
7 Mawu Ofanana  

Ndipo analipo ana atatu a Zeruya, ndiwo Yowabu, Abisai ndi Asahele. Ndipo Asahele anali waliwiro ngati mbawala.


Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa: Atero Davide mwana wa Yese, atero munthu wokwezedwa, ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo, ndi mwini nyimbo yokoma ya Israele.


iye adzakhala pamsanje; malo ake ochinjikiza adzakhala malinga amiyala; chakudya chake chidzapatsidwa kwa iye; madzi ake adzakhala chikhalire.


pomwepo udzakondwa mwa Yehova; ndipo Ine ndidzakuyendetsa pa misanje ya dziko lapansi; ndipo ndidzakudyetsa cholowa cha kholo lako Yakobo; pakuti pakamwa pa Yehova pananenapo.


Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga, asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, nadzandipondetsa pa misanje yanga.


Anamuyendetsa pa misanje ya dziko lapansi, ndipo anadya zipatso za m'minda; namyamwitsa uchi wa m'thanthwe, ndi mafuta m'mwala wansangalabwe;


Nsapato zako zikhale za chitsulo ndi mkuwa; ndipo monga masiku ako momwemo mphamvu yako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa