2 Samueli 22:33 - Buku Lopatulika33 Mulungu ndiye linga langa lamphamvu; ndipo Iye ayendetsa angwiro mu njira yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Mulungu ndiye linga langa lamphamvu; ndipo Iye ayendetsa angwiro mu njira yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Mulungu wathu ndiye linga langa lolimba, wandichotsera zoopsa m'njira zanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Ndi Mulungu amene anandipatsa mphamvu ndi kulungamitsa njira yanga. Onani mutuwo |