2 Samueli 22:32 - Buku Lopatulika32 Pakuti Mulungu ndani, koma Yehova? Ndipo thanthwe ndani, koma Mulungu wathu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Pakuti Mulungu ndani, koma Yehova? Ndipo thanthwe ndani, koma Mulungu wathu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 “Palibe Mulungu wina koma Chauta yekha. Palibe thanthwe lina lothaŵirapo koma Mulungu wathu yekha? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Mulungu wina ndi uti wofanana nanu Yehova? Ndipo ndani amene ndi Thanthwe kupatula Mulungu wathu? Onani mutuwo |