2 Samueli 22:30 - Buku Lopatulika30 Pakuti ndi Inu ndithamangira gulu; ndi Mulungu wanga ndilumphira linga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Pakuti ndi Inu ndithamangira gulu; ndi Mulungu wanga ndilumphira linga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ndi chithandizo chanu ndingathe kugonjetsa gulu la ankhondo. Ndi chithangato chanu, Inu Mulungu, ndingathe kupambana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndi thandizo lanu nditha kulimbana ndi gulu la ankhondo, ndi Mulungu wanga nditha kuchita zosatheka ndi munthu. Onani mutuwo |