2 Samueli 22:27 - Buku Lopatulika27 Ndi oyera mtima mudzadzionetsa woyera mtima; ndi otsutsatsutsa mudzadzionetsa wopotoza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndi oyera mtima mudzadzionetsa woyera mtima; ndi otsutsatsutsa mudzadzionetsa wopotoza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Kwa anthu oyera mtima mumadziwonetsa okoma mtima, koma kwa anthu oipa mtima mumadziwonetsa ochenjera koposa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Kwa woyera mtima, Inu mumaonetsa kuyera mtima kwanu, koma kwa anthu achinyengo mumaonetsanso kunyansidwa nawo. Onani mutuwo |