2 Samueli 22:26 - Buku Lopatulika26 Ndi chifundo Inu mudzadzionetsa wachifundo, ndi munthu wangwiro mudzadzionetsa wangwiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndi chifundo Inu mudzadzionetsa wachifundo, ndi munthu wangwiro mudzadzionetsa wangwiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 “Kwa anthu okhulupirika, Inu Mulungu mumadziwonetsa okhulupirika, kwa anthu aungwiro mumadziwonetsa abwino kotheratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Kwa wokhulupirika, Inu mumaonetsa kukhulupirika kwanu, kwa anthu amakhalidwe abwino, Inu mumaonetsanso makhalidwe abwino, Onani mutuwo |