2 Samueli 22:25 - Buku Lopatulika25 Chifukwa chake Yehova anandibwezera monga mwa cholungama changa; monga mwa kuyera kwanga pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Chifukwa chake Yehova anandibwezera monga mwa cholungama changa; monga mwa kuyera kwanga pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Nchifukwa chake Chauta wandipatsa mphotho molingana ndi kulungama kwanga, monga momwe akuwonera kuti ndilibe mlandu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Yehova wandipatsa mphotho molingana ndi chilungamo changa, molingana ndi makhalidwe anga abwino pamaso pake. Onani mutuwo |