2 Samueli 22:24 - Buku Lopatulika24 Ndinakhalanso wangwiro kwa Iye, ndipo ndinadzisunga kusachita kuipa kwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndinakhalanso wangwiro kwa Iye, ndipo ndinadzisunga kusachita kuipa kwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ndinalibe mlandu pamaso pake, ndinkalewa zoipa m'moyo wanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ndakhala moyo wosalakwa pamaso pake ndipo ndakhala ndi kupewa tchimo. Onani mutuwo |