2 Samueli 22:23 - Buku Lopatulika23 Pakuti maweruzo ake onse anali pamaso panga; ndipo za malemba ake, sindinawapatukire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Pakuti maweruzo ake onse anali pamaso panga; ndipo za malemba ake, sindinawapatukira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndidamvera malangizo ake onse, ndipo malamulo ake sindidaŵataye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Malamulo ake onse ali pamaso panga, sindinasiye malangizo ake. Onani mutuwo |