2 Samueli 22:19 - Buku Lopatulika19 Anandifikira ine tsiku la tsoka langa; koma Yehova anali mchirikizo wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Anandifikira ine tsiku la tsoka langa; koma Yehova anali mchirikizo wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Adaniwo adandithira nkhondo pamene ndinali m'mavuto, koma Chauta adandichirikiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Adaniwo analimbana nane pamene ndinali pa mavuto, koma Yehova anali thandizo langa. Onani mutuwo |