2 Samueli 22:18 - Buku Lopatulika18 Iye anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu, kwa iwo akudana ndi ine; pakuti anandiposa mphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Iye anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu, kwa iwo akudana ndi ine; pakuti anandiposa mphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adandipulumutsa kwa adani anga amphamvu, kwa onse amene ankadana nane; pakuti iwo anali amphamvu kwambiri kupambana ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu, adani anga amene anali amphamvu kuposa ine. Onani mutuwo |