2 Samueli 22:17 - Buku Lopatulika17 Iye anatumiza kuchokera kumwamba nanditenga; Iye ananditulutsa m'madzi aakulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Iye anatumiza kuchokera kumwamba nanditenga; Iye ananditulutsa m'madzi aakulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 “Ali kumwamba Chauta adatambalitsa dzanja nandigwira, ndi kundivuula m'madzi ozama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “Ali kumwamba, Iye anatambalitsa dzanja lake ndipo anandigwira; anandivuwula mʼmadzi ozama. Onani mutuwo |