2 Samueli 22:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Iye anatumiza mivi, nawawaza; mphezi, nawaopsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Iye anatumiza mivi, nawawaza; mphezi, nawaopsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Adaponya mivi yake, nabalalitsa adani ake. Adachititsa zing'aning'ani, naŵapirikitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Iye anaponya mivi yake, nabalalitsa adani ake, ndi zingʼaningʼani zake anawagonjetsa. Onani mutuwo |