2 Samueli 22:14 - Buku Lopatulika14 Yehova anagunda kumwamba; ndipo Wam'mwambamwamba ananena mau ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Yehova anagunda kumwamba; ndipo Wam'mwambamwamba ananena mau ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Kumwamba Chauta adagunda ngati bingu, Wopambanazonse liwu lake lidamveka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Yehova anabangula kumwamba ngati bingu, mawu a Wammwambamwamba anamveka ponseponse. Onani mutuwo |