2 Samueli 22:13 - Buku Lopatulika13 Cheza cha pamaso pake makala a moto anayaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Cheza cha pamaso pake makala a moto anayaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 M'kuŵala kumene kunali pamaso pake munkafumira makala amoto alaŵilaŵi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mʼkuwala kumene kunali pamaso pake munkachokera makala amoto alawilawi. Onani mutuwo |