2 Samueli 22:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anayesa mdimawo ngati mahema omzungulira Iye, kusonkhana kwa madzi ndi mitambo yochindikira ya mlengalenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anayesa mdimawo ngati mahema omzungulira Iye, kusonkhana kwa madzi ndi mitambo yochindikira ya mlengalenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mdima adausandutsa chofunda chake, mitambo yakuda yamvula adaisandutsa mwafuli wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iye anapanga mdima kukhala chofunda chake, mitambo yakuda ya mlengalenga. Onani mutuwo |