2 Samueli 22:10 - Buku Lopatulika10 Anaweramitsa miyambanso, natsika; ndipo mdima wandiweyani unali pansi pa mapazi ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Anaweramitsa miyambanso, natsika; ndipo mdima wandiweyani unali pansi pa mapazi ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Adang'amba thambo natsika pansi, mdima wabii unali ku mapazi ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iye anangʼamba thambo natsika pansi; pansi pa mapazi ake panali mitambo yakuda. Onani mutuwo |