2 Samueli 19:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anthu onse a m'mafuko onse a Israele analikutsutsana, ndi kuti, Mfumuyo inatilanditsa ife m'dzanja la adani athu, natipulumutsa m'dzanja la Afilisti; ndipo tsopano inathawa m'dziko kuthawa Abisalomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anthu onse a m'mafuko onse a Israele analikutsutsana, ndi kuti, Mfumuyo inatilanditsa ife m'dzanja la adani athu, natipulumutsa m'dzanja la Afilisti; ndipo tsopano inathawa m'dziko kuthawa Abisalomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo onsewo ankangokangana okhaokha. Ankati, “Mfumu Davide adatipulumutsa kwa adani athu, ndipo adatilanditsa kwa Afilisti. Koma tsopano watuluka m'dziko muno, kuthaŵa Abisalomu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakati pa mafuko onse a Israeli, anthu amakangana ndipo amati, “Mfumu inatipulumutsa mʼmanja mwa adani anthu. Iye ndi amene anatilanditsa mʼdzanja la Afilisti. Koma tsopano wathawa mʼdziko muno chifukwa cha Abisalomu. Onani mutuwo |